2 Mafumu 3:24 - Buku Lopatulika24 Ndipo pamene anafika ku misasa ya Israele, Aisraele ananyamuka, nakantha Amowabu, nathawa iwo pamaso pao; ndipo analowa m'dziko ndi kukantha Amowabu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ndipo pamene anafika ku misasa ya Israele, Aisraele ananyamuka, nakantha Amowabu, nathawa iwo pamaso pao; ndipo analowa m'dziko ndi kukantha Amowabu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Koma Amowabu aja atafika ku zithando za Aisraele, Aisraelewo adaŵathira nkhondo, iwowo nkuyamba kuthaŵa. Koma Aisraele aja ankapha Amowabuwo akuŵapirikitsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Koma Amowabu atafika ku misasa ya Israeli, Aisraeli ananyamuka ndi kumenyana nawo mpaka anathawa. Ndipo Aisraeli analowa mʼdzikolo ndi kupha Amowabu. Onani mutuwo |