Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mafumu 3:22 - Buku Lopatulika

22 Ndipo pamene anauka mamawa dzuwa linawala pamadzipo, naona Amowabu madzi ali pandunji pao ali psu ngati mwazi;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 Ndipo pamene anauka mamawa dzuwa linawala pamadzipo, naona Amowabu madzi ali pandunji pao ali psu ngati mwazi;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 Amowabuwo atadzuka m'mamaŵa pamene dzuŵa linkaŵala pa madzi, adaona madzi ali psuu ngati magazi kutsogolo kwao.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 Amowabu atadzuka mmamawa, dzuwa likuwala pa madziwo, anaona madziwo akuoneka wofiira ngati magazi patsogolo pawo.

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 3:22
3 Mawu Ofanana  

Atamva tsono Amowabu onse kuti adakwera mafumu aja kuthirana nao nkhondo, anamemeza onse akumanga lamba m'chuuno ndi okulapo, naima iwo m'malire.


nati, Uja ndi mwazi, atha kuonongana mafumu aja, anakanthana wina ndi mnzake; ndipo tsopano, tiyeni Amowabu inu, tikafunkhe.


Popeza Ambuye adamvetsa khamu la Aaramu phokoso la magaleta ndi mkokomo wa akavalo, phokoso la nkhondo yaikulu; nanenana wina ndi mnzake, Taonani mfumu ya Israele watimemezera mafumu a Ahiti ndi mafumu a Aejipito, atigwere.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa