2 Mafumu 3:17 - Buku Lopatulika17 Pakuti atero Yehova, Simudzaona mphepo, kapena kuona mvula, koma chigwacho chidzadzala ndi madzi; ndipo mudzamwa inu, ndi ng'ombe zanu, ndi zoweta zanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Pakuti atero Yehova, Simudzaona mphepo, kapena kuona mvula, koma chigwacho chidzadzala ndi madzi; ndipo mudzamwa inu, ndi ng'ombe zanu, ndi zoweta zanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Simudzaona mphepo kapena mvula, komabe mtsinje wopanda madziwu udzadzaza ndi madzi, ndipo inuyo mudzamwa, pamodzi ndi ng'ombe zanu ndi zoŵeta zanu zina zomwe.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Pakuti Yehova akunena kuti, ‘Simudzaona mphepo kapena mvula, komabe chigwa ichi chopanda madzi chidzadzaza ndi madzi, ndipo inu mudzamwa pamodzi ndi ngʼombe zanu ndiponso nyama zanu zonse.’ Onani mutuwo |