2 Mafumu 3:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo anati, Atero Yehova, Kumbani m'chigwa muno mukhale maenje okhaokha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo anati, Atero Yehova, Kumbani m'chigwa muno mukhale maenje okhaokha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Tsono adati, “Chauta akuti, ‘Mukumbe migwere mu mtsinje wopanda madziwu, ndipo Ine ndidzadzazamo madzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 ndipo anati, “Yehova akuti, ‘Kumbani ngalande mʼchigwa chonse.’ Onani mutuwo |