2 Mafumu 3:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo mfumu ya Israele inati, Kalanga ife! Pakuti Yehova waitana mafumu ife atatu kutipereka m'dzanja la Mowabu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo mfumu ya Israele inati, Kalanga ife! Pakuti Yehova waitana mafumu ife atatu kutipereka m'dzanja la Mowabu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Tsono mfumu Yoramu adati, “Kalanga ine! Chauta waitana mafumu atatufe, kuti atipereke m'manja mwa Amowabu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Mfumu inafuwula kuti, “Nʼchiyani chomwe chikutichitikira! Kodi Yehova wasonkhanitsa mafumu atatu pamodzi kuti atipereke mʼmanja mwa Amowabu?” Onani mutuwo |