Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mafumu 25:2 - Buku Lopatulika

2 Ndipo mzindawo unazingidwa ndi timalinga mpaka chaka chakhumi ndi chimodzi cha mfumu Zedekiya.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Ndipo mudziwo unazingidwa ndi timalinga mpaka chaka chakhumi ndi chimodzi cha mfumu Zedekiya.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Motero mzindawo udaazingidwa ndi zithandozo mpaka chaka cha 11 cha ufumu wa Zedekiya.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Mzindawo anawuzinga mpaka chaka cha khumi ndi chimodzi cha Mfumu Zedekiya.

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 25:2
6 Mawu Ofanana  

Nthawi ija anyamata a Nebukadinezara mfumu ya Babiloni anakwerera Yerusalemu, naumangira mzindawo misasa.


Ndipo kunali chaka chachisanu ndi chinai cha ufumu wake, mwezi wakhumi, tsiku lakhumi la mwezi, Nebukadinezara mfumu ya Babiloni, iye ndi khamu lake lonse anadzera Yerusalemu, naumangira misasa, naumangira timalinga mouzinga.


Tsiku lachisanu ndi chinai la mwezi wachinai njala idakula m'mzindamo, panalibe chakudya kwa anthu a m'dzikomo.


Mau amene anadza kwa Yeremiya kuchokera kwa Yehova chaka chakhumi cha Zedekiya mfumu ya Yuda, chimene chinali chaka chakhumi ndi chisanu ndi chitatu cha Nebukadinezara.


Ndipo mzinda unazingidwa mpaka chaka cha khumi ndi chimodzi cha mfumu Zedekiya.


Ndipo adzakuzingani m'midzi mwanu monse, kufikira adzagwa malinga anu aatali ndi olimba, amene munawakhulupirira, m'dziko lanu lonse; inde, adzakuzingani m'midzi mwanu monse, m'dziko lanu lonse limene Yehova Mulungu wanu akupatsani.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa