Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mafumu 24:9 - Buku Lopatulika

9 Nachita iye choipa pamaso pa Yehova, monga umo monse adachita atate wake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Nachita iye choipa pamaso pa Yehova, monga umo monse adachita atate wake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Yehoyakini adachita zoipa pamaso pa Chauta potsata zonse zimene ankachita bambo wake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Iye anachita zoyipa pamaso pa Yehova monga anachitira abambo ake.

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 24:9
5 Mawu Ofanana  

Ndipo anachita choipa pamaso pa Yehova, monga mwa zonyansa za amitundu amene Yehova anawaingitsa pamaso pa ana a Israele.


Nachita iye choipa pamaso pa Yehova, monga umo amachitira Manase atate wake.


Nayenda iye m'njira monse anayendamo atate wake, natumikira mafano anawatumikira atate wake, nawagwadira;


Nthawi ija anyamata a Nebukadinezara mfumu ya Babiloni anakwerera Yerusalemu, naumangira mzindawo misasa.


Ndipo unayendayenda pakati pa mikango, nukhala msona, nuphunzira kugwira nyama, nulusira anthu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa