Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mafumu 24:6 - Buku Lopatulika

6 Nagona Yehoyakimu ndi makolo ake, ndipo Yehoyakini mwana wake anakhala mfumu m'malo mwake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Nagona Yehoyakimu ndi makolo ake, ndipo Yehoyakini mwana wake anakhala mfumu m'malo mwake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Motero Yehoyakimu adamwalira, naikidwa m'manda. Ndipo Yehoyakini mwana wake adaloŵa ufumu m'malo mwake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Yehoyakimu anamwalira ndipo anayikidwa mʼmanda pamodzi ndi makolo ake. Ndipo Yehoyakini mwana wake analowa ufumu mʼmalo mwake.

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 24:6
7 Mawu Ofanana  

Machitidwe ena tsono a Yehoyakimu, ndi zonse anazichita, sizinalembedwe kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Yuda?


Nebukadinezara mfumu ya ku Babiloni anakwera kuyambana naye, nammanga ndi matangadza kumuka naye ku Babiloni.


Machitidwe ena tsono a Yehoyakimu, ndi zonyansa zake anazichita, ndi zija zidapezeka zomtsutsa; taonani, zilembedwa m'buku la mafumu a Israele ndi Yuda; ndi Yehoyakini mwana wake anakhala mfumu m'malo mwake.


Pali Ine, ati Yehova, ngakhale Koniya mwana wake wa Yehoyakimu mfumu ya Yuda akadakhala mphete ya padzanja langa lamanja, ndikadachotsa iwe kumeneko;


Chifukwa chake Yehova atero za Yehoyakimu mfumu ya Yuda: Adzasowa wokhala pa mpando wachifumu wa Davide; ndipo mtembo wake udzaponyedwa usana kunja kuli dzuwa, ndi usiku kuli chisanu.


Ndipo iwe, takwezera akalonga a Israele nyimbo ya maliro,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa