Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mafumu 24:5 - Buku Lopatulika

5 Machitidwe ena tsono a Yehoyakimu, ndi zonse anazichita, sizinalembedwe kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Yuda?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Machitidwe ena tsono a Yehoyakimu, ndi zonse anazichita, sizinalembedwa kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Yuda?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Tsono ntchito zina za Yehoyakimu ndi zonse zimene adazichita zidalembedwa m'buku la Mbiri ya Mafumu a ku Yuda.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Ntchito zina za Yehoyakimu ndi zonse zimene anachita, kodi sizinalembedwe mʼbuku la mbiri ya mafumu a Yuda?

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 24:5
7 Mawu Ofanana  

Tsono, machitidwe ake ena a Rehobowamu, ndi zonse anazichita, sizinalembedwe kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Yuda?


ndiponso chifukwa cha mwazi wosachimwa adaukhetsa; popeza anadzaza Yerusalemu ndi mwazi wosachimwa; ndipo Yehova sanafune kukhululukira.


Nagona Yehoyakimu ndi makolo ake, ndipo Yehoyakini mwana wake anakhala mfumu m'malo mwake.


Ndi machitidwe ena a Yoramu, ndi zonse anazichita, sizinalembedwe kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Yuda.


Machitidwe ena tsono a Yehoyakimu, ndi zonyansa zake anazichita, ndi zija zidapezeka zomtsutsa; taonani, zilembedwa m'buku la mafumu a Israele ndi Yuda; ndi Yehoyakini mwana wake anakhala mfumu m'malo mwake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa