Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mafumu 24:11 - Buku Lopatulika

11 Nafika Nebukadinezara mfumu ya Babiloni kumzinda, ataumangira misasa anyamata ake,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Nafika Nebukadinezara mfumu ya Babiloni kumudzi, ataumangira misasa anyamata ake,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Ndipo Nebukadinezara mfumu ya ku Babiloni adafika ku mzindawo pa nthaŵi imene ankhondo ake ankauzinga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 ndipo Nebukadinezara anafika ku mzindawo pamene ankhondo ake anawuzinga.

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 24:11
6 Mawu Ofanana  

Nthawi ija anyamata a Nebukadinezara mfumu ya Babiloni anakwerera Yerusalemu, naumangira mzindawo misasa.


Ndipo Yehoyakini mfumu ya Yuda anatulukira kwa mfumu ya Babiloni, iye ndi make, ndi anyamata ake, ndi akalonga ake, ndi adindo ake; mfumu ya Babiloni nimtenga chaka chachisanu ndi chitatu cha ufumu wake.


Ndipo ndidzamanga zithando kuzungulira iwe ponse, ndipo ndidzamanga linga ndi kuunjika miulu yakumenyanirana ndi iwe.


Kufikira ine ndidzadza, ndi kunka nanu kudziko lofanana ndi lanu, dziko la tirigu ndi vinyo, dziko la chakudya ndi minda yampesa.


Uziti, tsono kwa nyumba ya mpandukoyi, Simudziwa kodi izi nchiyani? Uziti, Taonani mfumu ya ku Babiloni inadza ku Yerusalemu, nkutenga mfumu yake ndi akalonga ake, nkubwera nao kuli iye ku Babiloni;


Pamenepo mitundu ya anthu inadzipereka kuukola kuchokera kumaiko a kumbali zonse, niuphimba ndi ukonde wao, nugwidwa uwu m'mbuna mwao.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa