2 Mafumu 23:9 - Buku Lopatulika9 Koma ansembe a misanje sanakwere kudza ku guwa la nsembe la Yehova ku Yerusalemu; koma anadya mkate wopanda chotupitsa pakati pa abale ao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Koma ansembe a misanje sanakwere kudza ku guwa la nsembe la Yehova ku Yerusalemu; koma anadya mkate wopanda chotupitsa pakati pa abale ao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Ansembe a ku akachisiwo sadaŵalole kufika ku guwa la Chauta ku Yerusalemu, komabe ankadya nao buledi wosatupitsa ndi ansembe anzao kumeneko. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Ngakhale kuti ansembe a ku malo opembedzera mafanowo sanawalole kuti atumikire pa guwa lansembe la Yehova mu Yerusalemu, koma ankadya buledi wopanda yisiti pamodzi ndi ansembe anzawo. Onani mutuwo |