2 Mafumu 23:22 - Buku Lopatulika22 Zedi silinachitike Paska lotere chiyambire masiku a oweruza anaweruza Israele, ngakhale m'masiku a mafumu a Israele, kapena mafumu a Yuda; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Zedi silinachitika Paska lotere chiyambire masiku a oweruza anaweruza Israele, ngakhale m'masiku a mafumu a Israele, kapena mafumu a Yuda; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Paska yotereyi inali isanachitikepo kuyambira nthaŵi ya aweruzi amene ankatsogolera Aisraele, kapena nthaŵi ya mafumu a ku Israele, kapenanso nthaŵi ya mafumu a ku Yuda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Paska yotere inali isanachitikepo kuyambira nthawi ya oweruza amene anatsogolera Israeli, kapenanso nthawi yonse ya mafumu a Yuda sipanachitikenso Paska ngati imeneyo. Onani mutuwo |