2 Mafumu 23:18 - Buku Lopatulika18 Nati iye, Mlekeni, munthu asakhudze mafupa ake. Naleka iwo mafupa ake akhale pamodzi ndi mafupa a mneneri uja anatuluka mu Samariya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Nati iye, Mlekeni, munthu asakhudze mafupa ake. Naleka iwo mafupa ake akhale pamodzi ndi mafupa a mneneri uja anatuluka m'Samariya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Yosiya adati, “Mlekeni. Munthu asachotse mafupa akewo ai.” Motero mafupawo adangoŵaleka pamodzi ndi mafupa a mneneri wa ku Samariya uja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Mfumuyo inati, “Alekeni manda amenewo, munthu asachotse mafupa ake.” Choncho anawasiya mafupa akewo pamodzi ndi mafupa a mneneri wa ku Samariya uja. Onani mutuwo |