Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mafumu 23:1 - Buku Lopatulika

1 Pamenepo mfumu inatumiza anthu, namsonkhanitsira akulu onse a Yuda ndi a mu Yerusalemu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Pamenepo mfumu inatumiza anthu, namsonkhanitsira akulu onse a Yuda ndi a m'Yerusalemu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Pamenepo mfumu Yosiya adatumiza mau kukaitana akuluakulu onse a ku Yuda ndi a ku Yerusalemu kuti adzasonkhane.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Pamenepo mfumu inayitanitsa akuluakulu onse a ku Yuda ndi Yerusalemu.

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 23:1
8 Mawu Ofanana  

Pambuyo pake Davide anamemezanso osankhika onse a mu Israele, anthu zikwi makumi atatu.


Nikwera mfumu kunka kunyumba ya Yehova, ndi amuna onse a Yuda, ndi onse okhala mu Yerusalemu pamodzi naye, ndi ansembe, ndi aneneri, ndi anthu onse aang'ono ndi aakulu; nawerenga iye m'makutu mwao mau onse a m'buku la chipangano adalipeza m'nyumba ya Yehova.


Pamenepo mfumu Hezekiya analawira mamawa, nasonkhanitsa akalonga a m'mzinda, nakwera kunka kunyumba ya Yehova.


Pakuti mfumu idapangana ndi akulu ake, ndi msonkhano wonse wa mu Yerusalemu, kuti achite Paska mwezi wachiwiri.


Yosiya ndiye wa zaka zisanu ndi zitatu polowa ufumu wake, nakhala mfumu mu Yerusalemu zaka makumi atatu mphambu chimodzi.


Ndisonkhanitsire akulu onse a mafuko anu, ndi akapitao anu, kuti ndinene mau awa m'makutu mwao, ndi kuchititsa mboni kumwamba ndi dziko lapansi zitsutse iwo.


Ndipo Yoswa anasonkhanitsa mafuko onse a Israele ku Sekemu, naitana akuluakulu a Israele ndi akulu ao, ndi oweruza ao, ndi akapitao ao; ndipo anadzionetsa pamaso pa Mulungu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa