Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mafumu 22:6 - Buku Lopatulika

6 kwa amisiri a mitengo, ndi omanga nyumba, ndi omanga linga; ndi kuti agule mitengo ndi miyala yosema kukonza nazo nyumbayi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 kwa amisiri a mitengo, ndi omanga nyumba, ndi omanga linga; ndi kuti agule mitengo ndi miyala yosema kukonza nazo nyumbayi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Ndiye kuti alipire amisiri a matabwa, amisiri omanga nyumba, amisiri omanga ndi miyala ndiponso amene adapereka mitengo ndi miyala yosema yokonzera Nyumbayo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 amisiri a matabwa, amisiri omanga ndi amisiri a miyala. Iwo akagulenso matabwa ndi miyala yosemedwa kuti akonzere Nyumba ya Yehova.

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 22:6
5 Mawu Ofanana  

Ndipo Hiramu mfumu ya Tiro anatumiza mithenga kwa Davide ndi mitengo yamkungudza, ndi amisiri a matabwa, ndi omanga nyumba; iwo nammangira Davide nyumba.


ndi omanga miyala ndi osema miyala, ndi kugula mitengo ndi miyala yosema kukakonza mogamuka nyumba ya Yehova, ndi zonse zoigulira nyumba zoikonzera.


ndizo zimene olindira pakhomo anasonkhetsa anthu; azipereke m'dzanja la antchito akuyang'anira nyumba ya Yehova; iwo azipereke kwa ogwira ntchito ya m'nyumba ya Yehova, akonze mogamuka nyumbayi,


Koma sanawawerengere ndalamazo zoperekedwa m'dzanja lao, pakuti anachita mokhulupirika.


Ndipo Davide anati asonkhanitse alendo okhala m'dziko la Israele; iye naika osema miyala afukule miyala, aiseme kuti amange nayo nyumba ya Mulungu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa