Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mafumu 21:25 - Buku Lopatulika

25 Machitidwe ena tsono a Amoni adawachita, sanalembedwe kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Yuda?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

25 Machitidwe ena tsono a Amoni adawachita, sanalembedwa kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Yuda?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

25 Tsono ntchito zonse zimene adachita Amoni zidalembedwa m'buku la Mbiri ya Mafumu a ku Yuda.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

25 Ntchito zina za Amoni ndi zonse zimene anachita, kodi sizinalembedwe mʼbuku la mbiri ya mafumu a Yuda?

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 21:25
6 Mawu Ofanana  

Tsono, machitidwe ake ena a Rehobowamu, ndi zonse anazichita, sizinalembedwe kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Yuda?


Machitidwe ena tsono a Hezekiya, ndi mphamvu yake yonse, ndi umo anamangira dziwe ndi mchera, nautengera mzinda madzi, sizinalembedwe kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Yuda?


Machitidwe ena tsono a Manase, ndi zochimwa zonse anazichita, sizinalembedwe kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Yuda?


Koma anthu a m'dzikomo anapha onse akumchitira chiwembu mfumu Amoni; ndipo anthu a m'dzikomo anamlonga ufumu Yosiya mwana wake m'malo mwake.


Naikidwa iye m'manda mwake m'munda wa Uza; nakhala mfumu m'malo mwake Yosiya mwana wake.


Ndi machitidwe ena a Yoramu, ndi zonse anazichita, sizinalembedwe kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Yuda.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa