Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mafumu 21:23 - Buku Lopatulika

23 Ndipo anyamata ake a Amoni anamchitira chiwembu, napha mfumuyo m'nyumba yakeyake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 Ndipo anyamata ake a Amoni anamchitira chiwembu, napha mfumuyo m'nyumba yakeyake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 Tsono anyamata ake adamchita chiwembu, namupha m'nyumba mwake momwe.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 Nduna za Amoni zinamuchita chiwembu ndipo zinamupha mʼnyumba yake.

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 21:23
8 Mawu Ofanana  

Ndipo Baasa mwana wa Ahiya, wa nyumba ya Isakara, anampangira chiwembu; ndipo Baasa anamkanthira ku Gibetoni wa Afilisti, popeza Nadabu ndi Aisraele onse adamangira misasa Gibetoni.


Ndipo mnyamata wake Zimiri, ndiye woyang'anira dera lina la magaleta ake, anampangira chiwembu; koma iye anali mu Tiriza kumwa ndi kuledzera m'nyumba ya Ariza, ndiye woyang'anira nyumba mu Tiriza.


Ndipo anyamata ake ananyamuka, napangana, nakantha Yowasi kunyumba ya Milo potsikira ku Sila.


Ndipo anamchitira chiwembu mu Yerusalemu, nathawira iye ku Lakisi; koma anatumiza akumtsata ku Lakisi, namupha komweko.


Ndipo Peka mwana wa Remaliya, kazembe wake, anamchitira chiwembu, nawakantha limodzi mfumu ndi Arigobu ndi Ariye mu Samariya, m'nsanja ya kunyumba ya mfumu; pamodzi ndi iye panali amuna makumi asanu a Giliyadi; ndipo anamupha, nakhala mfumu m'malo mwake.


Ndipo Hoseya mwana wa Ela anamchitira chiwembu Peka mwana wa Remaliya, namkantha, namupha, nakhala mfumu m'malo mwake chaka cha makumi awiri cha Yotamu mwana wa Uziya.


Koma pochiona ichi Ahaziya mfumu ya Yuda anathawa njira ya ku Betigahani. Namtsata Yehu, nati, Mumkanthe uyonso pagaleta; namkantha pa chikweza cha Guri chili pafupi pa Ibleamu. Nathawira iye ku Megido, namwalira komweko.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa