Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mafumu 20:7 - Buku Lopatulika

7 Nati Yesaya, Tenga nchinchi yankhuyu. Naitenga, naiika pafundo, nachira iye.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Nati Yesaya, Tenga nchinchi yankhuyu. Naitenga, naiika pafundo, nachira iye.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Pambuyo pake Yesaya adauza antchito a mfumu kuti, “Konzani phala lankhuyu. Kenaka mutengeko phalalo nkulimata pa chithupsa chake, kuti mfumu ichire.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Pamenepo Yesaya anati, “Konzani phala lankhuyu.” Iwo anakonza phalalo nalipaka pa chithupsacho ndipo Hezekiya anachira.

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 20:7
5 Mawu Ofanana  

Ndipo ndakuonjezera pa masiku ako zaka khumi ndi zisanu; ndidzakupulumutsa iwe ndi mzinda uno m'dzanja la mfumu ya Asiriya; ndidzatchinjiriza mzinda uno, chifukwa cha Ine ndekha, ndi chifukwa cha Davide mtumiki wanga.


Nati Hezekiya kwa Yesaya, Chizindikiro chake nchiyani kuti Yehova adzandichiza, ndi kuti ndidzakwera kunka kunyumba ya Yehova tsiku lachitatu?


Pamenepo anati, Bwera naoni ufa. Nathira m'nkhalimo; nati, Gawirani anthu kuti adye. Ndipo m'nkhalimo munalibe chowawa.


Ndipo Yesaya adati, Atenge m'bulu wankhuyu, auike pafundo, ndipo iye adzachira.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa