2 Mafumu 20:2 - Buku Lopatulika2 Pamenepo anatembenuzira nkhope yake kukhoma, napemphera kwa Yehova, ndi kuti, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Pamenepo anatembenuzira nkhope yake kukhoma, napemphera kwa Yehova, ndi kuti, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Pomwepo Hezekiya adatembenuka nayang'ana ku khoma, nayamba kupemphera kwa Chauta kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Hezekiya anatembenuka nayangʼana ku khoma ndipo anapemphera kwa Yehova kuti, Onani mutuwo |