2 Mafumu 2:22 - Buku Lopatulika22 Chotero madzi anachiritsidwa mpaka lero lino, monga mwa mau a Elisa ananenawo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Chotero madzi anachiritsidwa mpaka lero lino, monga mwa mau a Elisa ananenawo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Motero madziwo ngabwinobe kwambiri mpaka lero lino, potsata mau amene Elisa adaalankhula. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Kotero madziwo ndi abwino mpaka lero, molingana ndi mawu amene Elisa anayankhula. Onani mutuwo |