Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mafumu 2:18 - Buku Lopatulika

18 Nabwerera kwa iye ali chikhalire ku Yeriko, ndipo anati kwa iwo, Kodi sindinanene nanu, Musamuka?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 Nabwerera kwa iye ali chikhalire ku Yeriko, ndipo anati kwa iwo, Kodi sindinanena nanu, Musamuka?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Tsono adabwerera kwa Elisayo pamene iyeyo ankadikira ku Yeriko, ndipo iye adaŵauza kuti, “Kodi suja ndidaanena kuti musapite?”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 Atabwerera kwa Elisa (chifukwa anali akanali ku Yeriko), iye anawawuza kuti, “Kodi sindinakuwuzeni kuti musapite?”

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 2:18
3 Mawu Ofanana  

Koma anamuumiriza kufikira anachita manyazi; pamenepo anati, Tumizani. Motero anatumiza amuna makumi asanu, namfunafuna iwo masiku atatu, osampeza.


Ndipo amuna amumzinda anati kwa Elisa, Taonani, mumzinda muno m'mwabwino, monga umo aonera mbuye wanga; koma madzi ndi oipa, ndi nthaka siibalitsa.


Ndipo analowa, napyola pa Yeriko.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa