2 Mafumu 2:17 - Buku Lopatulika17 Koma anamuumiriza kufikira anachita manyazi; pamenepo anati, Tumizani. Motero anatumiza amuna makumi asanu, namfunafuna iwo masiku atatu, osampeza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Koma anamuumiriza kufikira anachita manyazi; pamenepo anati, Tumizani. Motero anatumiza amuna makumi asanu, namfunafuna iwo masiku atatu, osampeza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Koma adamkakamiza mpaka Elisayo mwamanyazi adaŵalola naŵauza kuti, “Chabwino, atumeni.” Ndiye iwo adaŵatuma anthu makumi asanuwo. Ndipo anthuwo adakafunafuna Eliya masiku atatu, koma osampeza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Koma anamukakamizabe mpaka Elisayo anachita manyazi moti sakanatha kukana. Choncho iye anati, “Atumizeni.” Ndipo anatumiza anthu makumi asanu amene anakafunafuna Eliya kwa masiku atatu koma sanamupeze. Onani mutuwo |