2 Mafumu 2:10 - Buku Lopatulika10 Nati iye, Wapempha chinthu chapatali, koma ukandipenya pamene ndichotsedwa kwa iwe, kudzatero nawe; koma ukapanda kundipenyapo, sikudzatero ai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Nati iye, Wapempha chinthu chapatali, koma ukandipenya pamene ndichotsedwa kwa iwe, kudzatero nawe; koma ukapanda kundipenyapo, sikudzatero ai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 “Eliya adauza Elisayo kuti, ‘Wapempha chinthu chapatali. Komabe ukandipenya pa nthaŵi imene ndikukusiya, zimene wapemphazi zidzakuchitikiradi. Koma ukapanda kundipenya, sizidzachitika.’ ” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Eliya anati, “Wapempha chinthu chapatali, komabe ukandiona pamene ndikuchotsedwa pamaso pako, mphamvu wapemphayi idzakhala yako, koma ukapanda kundiona sizidzachitika.” Onani mutuwo |