2 Mafumu 18:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo kunali chaka chachinai cha mfumu Hezekiya, ndicho chaka chachisanu ndi chiwiri cha Hoseya mwana wa Ela mfumu ya Israele Salimanezere mfumu ya Asiriya anakwerera Samariya, naumangira misasa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo kunali chaka chachinai cha mfumu Hezekiya, ndicho chaka chachisanu ndi chiwiri cha Hoseya mwana wa Ela mfumu ya Israele Salimanezere mfumu ya Asiriya anakwerera Samariya, naumangira misasa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Chaka chachinai cha ufumu wa Hezekiya chimene chinali chachisanu ndi chiŵiri cha ufumu wa Hoseya, mwana wa Ela, mfumu ya ku Israele, Salimanezere mfumu ya ku Asiriya adabwera kudzathira nkhondo mzinda wa Samariya, ndipo adauzinga ndi zithando zankhondo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Mʼchaka chachinayi cha Mfumu Hezekiya, chimene chinali chaka chachisanu ndi chiwiri cha Hoseya mwana wa Ela mfumu ya Israeli, Salimenezeri, mfumu ya ku Asiriya anabwera kudzathira nkhondo mzinda wa Samariya ndi kuwuzinga Onani mutuwo |