2 Mafumu 18:2 - Buku Lopatulika2 Ndiye wa zaka makumi awiri ndi zisanu polowa ufumu wake, nakhala mfumu zaka makumi awiri mphambu zisanu ndi zinai mu Yerusalemu; ndi dzina la make ndiye Abi mwana wa Zekariya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndiye wa zaka makumi awiri ndi zisanu polowa ufumu wake, nakhala mfumu zaka makumi awiri mphambu zisanu ndi zinai m'Yerusalemu; ndi dzina la make ndiye Abi mwana wa Zekariya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Anali wa zaka 25 pamene adaloŵa ufumu, ndipo adalamulira zaka 29 ku Yerusalemu. Mai wake anali Abi, mwana wa Zekariya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Anakhala mfumu ali ndi zaka 25 ndipo analamulira mu Yerusalemu zaka 29. Amayi ake anali Abi, mwana wa Zekariya. Onani mutuwo |