Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mafumu 17:5 - Buku Lopatulika

5 Pamenepo mfumu ya Asiriya anakwera m'dziko monse, nakwera ku Samariya, naumangira misasa zaka zitatu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Pamenepo mfumu ya Asiriya anakwera m'dziko monse, nakwera ku Samariya, naumangira misasa zaka zitatu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Nthaŵi yomweyo Salimanezere, mfumu ya ku Asiriya, adathira nkhondo dziko la Israele nakafika ku Samariya, nkukauzinga mzindawo ndi zithando zankhondo zaka zitatu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Mfumu ya ku Asiriya inapita kukathira nkhondo dziko lonse la Israeli ndipo inapita mpaka ku Samariya ndipo inazinga mzindawo kwa zaka zitatu.

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 17:5
6 Mawu Ofanana  

Koma mfumu ya Asiriya anampeza Hoseya alikuchita chiwembu; popeza anatuma mithenga kwa So mfumu ya ku Ejipito, osaperekanso mtulo kwa mfumu ya Asiriya, monga akachita chaka ndi chaka; chifukwa chake mfumu ya Asiriya anamtsekera, nammanga m'kaidi.


Ndipo kunali chaka chachinai cha mfumu Hezekiya, ndicho chaka chachisanu ndi chiwiri cha Hoseya mwana wa Ela mfumu ya Israele Salimanezere mfumu ya Asiriya anakwerera Samariya, naumangira misasa.


Ndipo zitatha izi, Benihadadi mfumu ya Aramu anamemeza khamu lake lonse, nakwera, namangira misasa Samariya.


Samariya adzasanduka wabwinja, pakuti anapandukana ndi Mulungu wake; iwo adzagwa ndi lupanga, ana ao amakanda adzaphwanyika, ndi akazi ao okhala ndi pakati adzatumbulidwa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa