Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mafumu 17:1 - Buku Lopatulika

1 Chaka chakhumi ndi ziwiri cha Ahazi mfumu ya Yuda Hoseya mwana wa Ela analowa ufumu wake wa Israele mu Samariya, nakhala mfumu zaka zisanu ndi zinai.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Chaka chakhumi ndi ziwiri cha Ahazi mfumu ya Yuda Hoseya mwana wa Ela analowa ufumu wake wa Israele m'Samariya, nakhala mfumu zaka zisanu ndi zinai.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Chaka cha 12 cha ufumu wa Ahazi mfumu ya ku Yuda, Hoseya mwana wa Ela adaloŵa ufumu wa ku Israele ku Samariya. Ndipo adalamulira zaka zisanu ndi zinai.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Mʼchaka cha 12 cha Ahazi mfumu ya Yuda, Hoseya mwana wa Ela anakhala mfumu ya Israeli mu Samariya ndipo analamulira zaka zisanu ndi zinayi.

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 17:1
4 Mawu Ofanana  

Ndipo Hoseya mwana wa Ela anamchitira chiwembu Peka mwana wa Remaliya, namkantha, namupha, nakhala mfumu m'malo mwake chaka cha makumi awiri cha Yotamu mwana wa Uziya.


Chaka chakhumi mphambu zisanu ndi ziwiri cha Peka mwana wa Remaliya Ahazi mwana wa Yotamu mfumu ya Yuda analowa ufumu wake.


Nachita iye choipa pamaso pa Yehova, koma osati monga mafumu a Israele asanakhale iye.


Ndipo kunali chaka chachitatu cha Hoseya mwana wa Ela mfumu ya Israele, Hezekiya mwana wa Ahazi mfumu ya Yuda analowa ufumu wake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa