2 Mafumu 16:6 - Buku Lopatulika6 Nthawi yomweyo Rezini mfumu ya Aramu anabwezera Elati kwa Aramu, napirikitsa Ayuda ku Elati; nadza Aaramu ku Elati, nakhala komwemo kufikira lero lino. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Nthawi yomweyo Rezini mfumu ya Aramu anabwezera Elati kwa Aramu, napirikitsa Ayuda ku Elati; nadza Aaramu ku Elati, nakhala komwemo kufikira lero lino. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Nthaŵi imeneyo Rezini mfumu ya ku Edomu adapirikitsa Ayuda ku Elati, nalanda mzindawo, kuubwezera kwa Aedomu, ndipo iwo adakhala kumeneko mpaka lero lino. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Nthawi imeneyo Rezini mfumu ya Aramu anatenganso Elati ndi kumubwezera kwa Aaramu, nathamangitsa anthu a ku Yuda mu Elatimo. Aedomu anapita kukakhala ku Elati ndipo akukhalako mpaka lero lino. Onani mutuwo |