2 Mafumu 16:2 - Buku Lopatulika2 Ahazi anali wa zaka makumi awiri polowa ufumu wake, nakhala mfumu zaka khumi mphambu zisanu ndi chimodzi mu Yerusalemu; koma sanachite zoongoka pamaso pa Yehova Mulungu wake, ngati Davide kholo lake; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ahazi anali wa zaka makumi awiri polowa ufumu wake, nakhala mfumu zaka khumi mphambu zisanu ndi chimodzi m'Yerusalemu; koma sanachite zoongoka pamaso pa Yehova Mulungu wake, ngati Davide kholo lake; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Ahazi anali wa zaka 20 pamene adaloŵa ufumu ndipo adalamulira zaka 16 ku Yerusalemu. Iyeyo sadachite zolungama pamaso pa Chauta monga m'mene Davide kholo lake ankachitira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Ahazi anakhala mfumu ali ndi zaka makumi awiri ndipo analamulira mu Yerusalemu zaka 16. Iye sanachite zabwino pamaso pa Yehova Mulungu wake monga momwe Davide kholo lake ankachitira. Onani mutuwo |