2 Mafumu 15:7 - Buku Lopatulika7 Nagona Azariya ndi makolo ake, namuika ndi makolo ake m'mzinda wa Davide; nakhala mfumu m'malo mwake Yotamu mwana wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Nagona Azariya ndi makolo ake, namuika ndi makolo ake m'mudzi wa Davide; nakhala mfumu m'malo mwake Yotamu mwana wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Ndipo adamwalira naikidwa m'manda momwe adaikidwa makolo akewo mu mzinda wa Davide. Ndiye Yotamu mwana wake adaloŵa ufumu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Azariya anamwalira ndipo anayikidwa mʼmanda pamodzi ndi makolo ake mu Mzinda wa Davide. Ndipo Yotamu mwana wake analowa ufumu mʼmalo mwake. Onani mutuwo |