2 Mafumu 15:6 - Buku Lopatulika6 Machitidwe ena tsono a Azariya, ndi zonse anazichita, sizinalembedwe kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Yuda? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Machitidwe ena tsono a Azariya, ndi zonse anazichita, sizinalembedwa kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Yuda? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Tsono ntchito zina za Azariya ndi zonse zimene adazichita, zidalembedwa m'buku la Mbiri ya Mafumu a ku Yuda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Ntchito zina za Azariya ndi zonse zimene anachita, kodi sizinalembedwe mʼbuku la mbiri ya mafumu a Yuda? Onani mutuwo |