Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mafumu 15:36 - Buku Lopatulika

36 Machitidwe ena tsono a Yotamu, ndi zonse anazichita, sizinalembedwe kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Yuda?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

36 Machitidwe ena tsono a Yotamu, ndi zonse anazichita, sizinalembedwa kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Yuda?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

36 Tsono ntchito zina za Yotamu, ndi zonse zimene ankachita, zidalembedwa m'buku la Mbiri ya Mafumu a ku Yuda.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

36 Ntchito zina za Yotamu ndi zonse zimene anachita, kodi sizinalembedwe mʼbuku la mbiri ya mafumu a Yuda?

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 15:36
6 Mawu Ofanana  

Tsono, machitidwe ake ena a Rehobowamu, ndi zonse anazichita, sizinalembedwe kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Yuda?


Komatu sanaichotse misanje; anthu anapherabe nsembe, nafukiza pamisanje. Iye anamanga chipata cha kumtunda cha nyumba ya Yehova.


Masiku awa Yehova anayamba kutumizira Yuda Rezini mfumu ya Aramu, ndi Peka mwana wa Remaliya, amenyane naye.


Ndi machitidwe ena a Yoramu, ndi zonse anazichita, sizinalembedwe kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Yuda.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa