2 Mafumu 15:34 - Buku Lopatulika34 Nachita iye zoongoka pamaso pa Yehova; anachita monga mwa zonse anazichita atate wake Uziya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Nachita iye zoongoka pamaso pa Yehova; anachita monga mwa zonse anazichita atate wake Uziya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Yotamu adachita zolungama pamaso pa Chauta ndipo kutsata zonse zimene ankachita Uziya bambo wake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Iye anachita zabwino pamaso pa Yehova monga anachitira Uziya abambo ake. Onani mutuwo |