2 Mafumu 15:3 - Buku Lopatulika3 Nachita iye zoongoka pamaso pa Yehova, monga mwa zonse adazichita atate wake Amaziya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Nachita iye zoongoka pamaso pa Yehova, monga mwa zonse adazichita atate wake Amaziya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Azariya adachita zolungama pamaso pa Chauta, monga momwe ankachitira bambo wake Amaziya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Iyeyo anachita zabwino pamaso pa Yehova, monga momwe anachitira Amaziya abambo ake. Onani mutuwo |