Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mafumu 15:22 - Buku Lopatulika

22 Nagona Menahemu ndi makolo ake; nakhala mfumu m'malo mwake Pekahiya mwana wake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 Nagona Menahemu ndi makolo ake; nakhala mfumu m'malo mwake Pekahiya mwana wake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 Ndipo Menahemu adamwalira, naikidwa m'manda momwe adaikidwa makolo akewo. Tsono Pekahiya mwana wake adaloŵa ufumu m'malo mwake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 Menahemu anamwalira ndipo anayikidwa mʼmanda pamodzi ndi makolo ake. Ndipo Pekahiya mwana wake analowa ufumu mʼmalo mwake.

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 15:22
3 Mawu Ofanana  

Ndipo Salumu mwana wa Yabesi anamchitira chiwembu, namkantha pamaso pa anthu, namupha; nakhala mfumu m'malo mwake.


Machitidwe ena tsono a Menahemu, ndi zonse anazichita, sizinalembedwe kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Israele?


Chaka cha makumi asanu a Azariya mfumu ya Yuda, Pekahiya mwana wa Menahemu analowa ufumu wake wa Israele mu Samariya, nakhala mfumu zaka ziwiri.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa