Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mafumu 15:21 - Buku Lopatulika

21 Machitidwe ena tsono a Menahemu, ndi zonse anazichita, sizinalembedwe kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Israele?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

21 Machitidwe ena tsono a Menahemu, ndi zonse anazichita, sizinalembedwa kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Israele?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

21 Tsono ntchito zina za Menahemu, ndi zonse zimene adazichita, zidalembedwa m'buku la Mbiri ya Mafumu a ku Israele.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

21 Ntchito zina za Menahemu ndi zonse zimene anachita, kodi sizinalembedwe mʼbuku la mbiri ya mafumu a Israeli?

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 15:21
5 Mawu Ofanana  

Ndipo machitidwe ena a Yerobowamu m'mene umo anachitira ufumu, taona, analembedwa m'buku la machitidwe a mafumu a Israele.


Machitidwe ake ena tsono adawachita Ahaziya, sanalembedwe kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Israele?


Ndipo Menahemu anasonkhetsa Israele ndalamazi, nasonkhetsa achuma, yense masekeli makumi asanu a siliva, kuti azipereke kwa mfumu ya Asiriya. Nabwerera mfumu ya Asiriya osakhala m'dzikomo.


Nagona Menahemu ndi makolo ake; nakhala mfumu m'malo mwake Pekahiya mwana wake.


Akachimwira Inu (pakuti palibe munthu wosachimwa), nimukakwiya nao, ndi kuwapereka kwa adani, kuti awatenge andende kunka nao ku dziko lakutali, kapena lapafupi;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa