2 Mafumu 15:2 - Buku Lopatulika2 Anali wa zaka khumi ndi zisanu ndi chimodzi polowa ufumu wake, nakhala mfumu zaka makumi asanu mphambu ziwiri mu Yerusalemu; ndi dzina la make ndiye Yekoliya wa ku Yerusalemu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Anali wa zaka khumi ndi zisanu ndi chimodzi polowa ufumu wake, nakhala mfumu zaka makumi asanu mphambu ziwiri m'Yerusalemu; ndi dzina la make ndiye Yekoliya wa ku Yerusalemu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Iyeyu anali wa zaka 16 pamene adaloŵa ufumu, ndipo adalamulira zaka 52 ku Yerusalemu. Mai wake anali Yekoliya wa ku Yerusalemu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Iye anakhala mfumu ali ndi zaka 16 ndipo analamulira mu Yerusalemu zaka 52. Amayi ake anali Yekoliya wa ku Yerusalemu. Onani mutuwo |