Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mafumu 15:11 - Buku Lopatulika

11 Machitidwe ena tsono a Zekariya, taonani, zalembedwa m'buku la machitidwe a mafumu a Israele.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Machitidwe ena tsono a Zekariya, taonani, zalembedwa m'buku la machitidwe a mafumu a Israele.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Tsono ntchito zonse zimene adachita Zekariya zidalembedwa m'buku la Mbiri ya Mafumu a Israele.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Ntchito zina za Zekariya, zinalembedwa mʼbuku la mbiri ya mafumu a Israeli.

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 15:11
6 Mawu Ofanana  

Ndipo machitidwe ena a Yerobowamu m'mene umo anachitira ufumu, taona, analembedwa m'buku la machitidwe a mafumu a Israele.


Machitidwe ake ena tsono adawachita Ahaziya, sanalembedwe kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Israele?


Machitidwe ena tsono a Yerobowamu, ndi zonse anazichita, ndi mphamvu yake, umo anachita nkhondo, nabweza kwa Israele Damasiko ndi Hamati amene anali a Yuda, sizinalembedwe kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Israele?


Ndipo Salumu mwana wa Yabesi anamchitira chiwembu, namkantha pamaso pa anthu, namupha; nakhala mfumu m'malo mwake.


Awa ndi mau a Yehova anawanena ndi Yehu, ndi kuti, Ana ako kufikira mbadwo wachinai adzakhala pa mpando wachifumu wa Israele. Ndipo kunatero momwemo.


Machitidwe ena tsono a Salumu ndi chiwembu chake anachichita, taonani, zalembedwa m'buku la machitidwe a mafumu a Israele.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa