2 Mafumu 14:8 - Buku Lopatulika8 Pamenepo Amaziya anatuma mithenga kwa Yehowasi mwana wa Yehowahazi mwana wa Yehu mfumu ya Israele, ndi kuti, Idzani tionane maso. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Pamenepo Amaziya anatuma mithenga kwa Yehowasi mwana wa Yehowahazi mwana wa Yehu mfumu ya Israele, ndi kuti, Idzani tionane maso. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Nthaŵi ina Amaziya adatuma amithenga kwa Yehowasi mwana wa Yehowahazi, mdzukulu wa Yehu, mfumu ya ku Israele, kukanena momputa kuti, “Ubwere kuno, tidzaonane maso ndi maso.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Tsono Amaziya anatuma amithenga kwa Yehowasi mwana wa Yehowahazi, mwana wa Yehu mfumu ya Israeli ndi kumuopseza kuti, “Bwera tidzaonane maso ndi maso.” Onani mutuwo |