2 Mafumu 14:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo kunali, utakhazikika ufumu m'dzanja lake, anakantha anyamata ake amene adakantha mfumu atate wake; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo kunali, utakhazikika ufumu m'dzanja lake, anakantha anyamata ake amene adakantha mfumu atate wake; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Atangolandira mphamvu zonse zaufumu m'manja mwake, Amaziya adapha anyamata ake amene adaapha mfumu ija, bambo wake. Koma ana a anthuwo sadaŵaphe, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Atakhazikika mu ufumu wake, Amaziya anapha atumiki ake amene anapha abambo ake, mfumu ija. Onani mutuwo |