2 Mafumu 14:4 - Buku Lopatulika4 Koma misanje sanaichotse; anthu anapherabe nsembe, nafukiza pamisanje. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Koma misanje sanaichotse; anthu anapherabe nsembe, nafukiza pamisanje. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Koma akachisi opembedzerako mafano pa zitunda sadaŵaononge. Anthu adapitirirabe kupereka nsembe ndi kumafukiza lubani pa malo amenewo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Komabe sanachotse malo opembedzerapo mafano. Anthu anapitiriza kupereka nsembe ndi kufukiza lubani kumeneko. Onani mutuwo |