2 Mafumu 14:2 - Buku Lopatulika2 Ndiye wa zaka makumi awiri ndi zisanu polowa ufumu; nakhala mfumu zaka makumi awiri mphambu zisanu ndi zinai mu Yerusalemu; dzina la make ndiye Yehowadani wa ku Yerusalemu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndiye wa zaka makumi awiri ndi zisanu polowa ufumu; nakhala mfumu zaka makumi awiri mphambu zisanu ndi zinai m'Yerusalemu; dzina la make ndiye Yehowadani wa ku Yerusalemu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Iyeyo anali wa zaka 25 pamene adaloŵa ufumu, ndipo adalamulira zaka 29 ku Yerusalemu. Mai wake anali Yehowadani wa ku Yerusalemu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Iye anali ndi zaka 25 pamene anakhala mfumu ndipo analamulira mu Yerusalemu zaka 29. Amayi ake anali Yehoyadini wa ku Yerusalemu. Onani mutuwo |