Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mafumu 14:18 - Buku Lopatulika

18 Machitidwe ena tsono a Amaziya, sanalembedwe kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Yuda?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 Machitidwe ena tsono a Amaziya, sanalembedwa kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Yuda?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Tsono ntchito zina zonse zimene adachita Amaziya zidalembedwa m'buku la Mbiri ya Mafumu a ku Yuda.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 Ntchito zina za Amaziya, kodi sizinalembedwe mʼbuku la mbiri ya mafumu a Yuda?

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 14:18
7 Mawu Ofanana  

Ndipo machitidwe otsiriza a Solomoni, ndi ntchito zake zonse anazichita, ndi nzeru zake, sizinalembedwe kodi m'buku la machitidwe a Solomoni?


Tsono, machitidwe ake ena a Rehobowamu, ndi zonse anazichita, sizinalembedwe kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Yuda?


Machitidwe ena tsono a Yowasi, ndi zonse anazichita, ndi mphamvu yake yochita nkhondo nayo pa Amaziya mfumu ya Yuda, sizinalembedwe kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Israele?


Machitidwe ena tsono a Yehowahazi, ndi zonse anazichita, ndi mphamvu yake, sizinalembedwe kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Israele?


Ndipo Amaziya mwana wa Yowasi mfumu ya Yuda anakhala ndi moyo, atamwalira Yehowasi mwana wa Yehowahazi mfumu ya Israele, zaka khumi ndi zisanu.


Ndipo anamchitira chiwembu mu Yerusalemu, nathawira iye ku Lakisi; koma anatumiza akumtsata ku Lakisi, namupha komweko.


Ndi machitidwe ena a Yoramu, ndi zonse anazichita, sizinalembedwe kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Yuda.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa