2 Mafumu 13:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo Yehowahazi anagona ndi makolo ake, namuika mu Samariya; nakhala mfumu m'malo mwake Yowasi mwana wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo Yehowahazi anagona ndi makolo ake, namuika m'Samariya; nakhala mfumu m'malo mwake Yowasi mwana wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Motero Yehowahazi adamwalira, naikidwa m'manda momwe adaikidwa makolo akewo ku Samariya. Tsono Yehowasi mwana wake adaloŵa ufumu m'malo mwake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Yehowahazi anamwalira ndipo anayikidwa mʼmanda mu Samariya. Ndipo Yowasi mwana wake analowa ufumu mʼmalo mwake. Onani mutuwo |