Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mafumu 13:8 - Buku Lopatulika

8 Machitidwe ena tsono a Yehowahazi, ndi zonse anazichita, ndi mphamvu yake, sizinalembedwe kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Israele?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Machitidwe ena tsono a Yehowahazi, ndi zonse anazichita, ndi mphamvu yake, sizinalembedwa kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Israele?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Tsono ntchito zina za Yehowahazi pamodzi ndi zimene adazichita, zidalembedwa m'buku la Mbiri ya Mafumu a ku Israele.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Ntchito zina za Yehowahazi ndi zonse zimene anachita, kodi sizinalembedwe mʼbuku la mbiri ya mafumu a Israeli?

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 13:8
8 Mawu Ofanana  

Ndipo kunali, atakalamba Solomoni, akazi ake anapambutsa mtima wake atsate milungu ina; ndipo mtima wake sunakhale wangwiro ndi Yehova Mulungu wake monga mtima wa Davide atate wake.


Tsono, machitidwe ake ena a Rehobowamu, ndi zonse anazichita, sizinalembedwe kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Yuda?


Nagona Rehobowamu ndi makolo ake, naikidwa kwa makolo ake m'mzinda wa Davide. Ndipo dzina la amake linali Naama Mwamoni, nalowa ufumu m'malo mwake Abiya mwana wake.


Machitidwe ake ena tsono adawachita Ahaziya, sanalembedwe kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Israele?


Koma mfumu ya Aramu sanasiyire Yehowahazi anthu, koma apakavalo makumi asanu, ndi magaleta khumi, ndi oyenda pansi zikwi khumi; popeza mfumu ya Aramu anawaononga, nawayesa ngati fumbi lopondapo.


Ndipo Yehowahazi anagona ndi makolo ake, namuika mu Samariya; nakhala mfumu m'malo mwake Yowasi mwana wake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa