2 Mafumu 13:16 - Buku Lopatulika16 Nati kwa mfumu ya Israele, Pingiridzani. Napingiridza. Ndipo Elisa anasanjika manja ake pa manja a mfumu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Nati kwa mfumu ya Israele, Pingiridzani. Napingiridza. Ndipo Elisa anasanjika manja ake pa manja a mfumu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Tsono Elisa adauza Yehowasi mfumu ya ku Israeleyo kuti, “Kokani utawu.” Iye nkukokadi. Apo Elisayo adaika manja ake pa manja a mfumuyo, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Elisa anawuza mfumu ya Israeli kuti, “Tenga uta mʼdzanja lako.” Pamene anatenga utawo, Elisa anayika manja ake pa manja a mfumuyo. Onani mutuwo |