Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mafumu 13:15 - Buku Lopatulika

15 Nanena naye Elisa, Tenga uta ndi mivi; nadzitengera uta ndi mivi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 Nanena naye Elisa, Tenga uta ndi mivi; nadzitengera uta ndi mivi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 Pamenepo Elisa adauza Yehowasi kuti, “Tengani uta ndi mivi yake.” Adatenga utawo ndi miviyo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 Elisa anamuwuza kuti, “Tenga uta ndi mivi.” Ndipo anaterodi.

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 13:15
3 Mawu Ofanana  

Ndipo Elisa anadwala nthenda ija adafa nayo, namtsikira Yehowasi mfumu ya Israele, namlirira, nati, Atate wanga, atate wanga, galeta wa Israele ndi apakavalo ake!


Nati kwa mfumu ya Israele, Pingiridzani. Napingiridza. Ndipo Elisa anasanjika manja ake pa manja a mfumu.


Ndipo anadza kwa ife natenga lamba la Paulo, nadzimanga yekha manja ndi mapazi, nati, Atero Mzimu Woyera, Munthu mwini lamba ili, adzammanga kotero Ayuda a mu Yerusalemu, nadzampereka m'manja a amitundu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa