Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Mafumu 12:2 - Buku Lopatulika

2 Ndipo Yowasi anachita zoongoka pamaso pa Yehova masiku ake onse, m'mene anamlangizira wansembe Yehoyada.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Ndipo Yowasi anachita zoongoka pamaso pa Yehova masiku ake onse, m'mene anamlangizira wansembe Yehoyada.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Tsono Yowasiyo adachita zolungama pamaso pa Chauta masiku onse a moyo wake, chifukwa choti Yehoyada, wansembe uja, ankamlangiza.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Yowasi anachita zolungama pamaso pa Yehova masiku onse amene wansembe Yehoyada ankamulangiza.

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 12:2
8 Mawu Ofanana  

Chaka chachisanu ndi chiwiri cha Yehu, Yowasi analowa ufumu wake; nakhala mfumu mu Yerusalemu zaka makumi anai; ndi dzina la mai wake ndiye Zibiya wa ku Beereseba.


Koma misanje sanaichotse; anthu anapherabe nsembe, nafukiza kumisanje.


Pamenepo mfumu Yowasi anaitana Yehoyada wansembe, ndi ansembe ena, nanena nao, Mulekeranji kukonza mogamuka nyumba? Tsono musalandiranso ndalama kwa anzanu odziwana nao, kuziperekera mogamuka nyumba.


Ndipo anachita zoongoka pamaso pa Yehova, koma wosanga Davide kholo lake; nachita monga mwa zonse anazichita Yowasi atate wake.


Ndipo Yowasi anachita zoongoka pamaso pa Yehova masiku onse a Yehoyada wansembe.


Ndipo anachita zoongoka pamaso pa Yehova, koma wosachita ndi mtima wangwiro.


Nachita iye zoongoka pamaso pa Yehova, monga mwa zonse adazichita atate wake Amaziya.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa