2 Mafumu 12:16 - Buku Lopatulika16 Ndalama za nsembe zopalamula ndi ndalama za nsembe yauchimo sanabwere nazo kunyumba ya Yehova; nza ansembe izi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndalama za nsembe zopalamula ndi ndalama za nsembe yauchimo sanabwere nazo kunyumba ya Yehova; nza ansembe izi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Ndalama zoperekera nsembe zolipira mlandu ndiponso ndalama zoperekera nsembe zopepesera machimo, sankaziponya m'bokosi la m'Nyumba ya Chauta. Zimenezo zinali za ansembe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Ndalama zomwe zinkaperekedwa pa nsembe yopepesera machimo ndi nsembe yoperekedwa chifukwa cha tchimo sanabwere nazo ku Nyumba ya Yehova pakuti zinali za ansembe. Onani mutuwo |