2 Mafumu 12:11 - Buku Lopatulika11 Napereka ndalama zoyesedwa m'manja mwa iwo akuchita ntchitoyi, akuyang'anira nyumba ya Yehova; ndipo iwo analipira nazo amisiri a mitengo ndi omanga, akugwira ntchito ya pa nyumba ya Yehova, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Napereka ndalama zoyesedwa m'manja mwa iwo akuchita ntchitoyi, akuyang'anira nyumba ya Yehova; ndipo iwo analipira nazo amisiri a mitengo ndi omanga, akugwira ntchito ya pa nyumba ya Yehova, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Tsono ndalamazo ataziyesa, ankazipereka kwa akapitao okonzetsa Nyumba ya Chauta aja. Iwowo ankalipira amisiri a matabwa ndi amisiri omanga nyumba, amene ankagwira ntchito yokonza Nyumba ya Chautayo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Ankati akadziwa kuti ndalamazo zilipo zingati, ankazipereka kwa anthu amene ankayangʼanira ntchito yokonza nyumbayo. Ndalamazo ankalipira anthu amene ankagwira ntchito yokonza Nyumba ya Yehova, amisiri a matabwa ndi amisiri omanga nyumba, Onani mutuwo |